Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Analemba Baibulo Ndi Ndani?

Kodi Analemba Baibulo Ndi Ndani?

Ngati Baibulo linalembedwa ndi anthu, n’chifukwa chiyani limatchulidwa kuti ndi “mawu a Mulungu?” (1 Atesalonika 2:13) Kodi Mulungu anauza bwanji anthu zoyenera kulemba m’Baibulo?