Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mulungu Ali Ndi Dzina?

Kodi Mulungu Ali Ndi Dzina?

Mulungu ali ndi maina ambiri audindo monga akuti Atate, Mlengi ndi Ambuye. (Yobu 34:12; Mlaliki 12:1; Danieli 2:47) Koma kodi ali ndi dzina lakelake?