Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mulungu Amavomereza Zipembedzo Zonse?

Kodi Mulungu Amavomereza Zipembedzo Zonse?

Kodi zipembedzo zonse zimaphunzitsa zoona? Ngati zili choncho, n’chifukwa chiyani anthu amakhulupirira zinthu zosiyanasiyana? Nanga tingadziwe bwanji kuti tili m’chipembedzo choona chomwe Mulungu amachivomereza?