Pulogalamu ya Msonkhano wa 2020

Pulogalamu ya Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2020 wakuti, ‘Kondwerani Nthawi Zonse.’

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Afilipi 4:4​—“Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye. Ndibwerezanso, Kondwerani.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Salimo 105:3​—“Nyadirani dzina lake loyera. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Salimo 37:4​—“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza anthu amene abwera pamsonkhano.