Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira

Kodi mnzanu kapena m’bale wanu anamwalira ndipo mukufunikira kulimbikitsidwa?

Mawu Oyamba

Kabukuka kali ndi mfundo za m’Baibulo zothandiza munthu amene waferedwa.

“Sizingakhale Zoona!”

Tsiku lililonse mabanja padziko lonse amakumana ndi zinthu zokhumudwitsa.

Kodi Nkwachibadwa Kumva Mwanjira Imeneyi?

Ngati mwaferedwa, kodi n’kulakwa kusonyeza kuti muli ndi chisoni?

Kodi Ndingakhale Motani Ndi Chisoni Changa?

Kodi tiyenera kubisa zoti tili ndi chisoni?

Kodi Ena Angathandize Motani?

Anzake a munthu amene waferedwa akazindikira zimene munthuyo akufunika, angachite bwino kumulimbikitsa komanso kumuthandiza, osachita kudikira kuti munthuyo awapemphe.

Chiyembekezo Chotsimikizirika cha Akufa

Munthu amene tinkamukonda akamwalira, zimakhala zowawa ukaganizira kuti sudzathanso kulankhula naye kapena kuseka naye. Koma Baibulo limatithandiza kukhala ndi chiyembekezo.