Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2020-2021​—Wokhala ndi Woyang’anira Dera

Gwiritsani ntchito pulogalamuyi potsatira nkhani zimene zikukambidwa pamsonkhano waderawu. Mutu wamsonkhanowu ndi wakuti “Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!”

Muzisangalatsa Mtima wa Yehova!

Pulogalamu ya nkhani za m’mawa komanso za masana pamsonkhano wadera wokhala ndi woyang’anira dera.

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mafunso amenewa adzayankhidwa pamene nkhani zikukambidwa.