Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2020-2021​—Wokhala ndi Woimira Nthambi

Onani pulogalamu ya msonkhano wadera umenewu. Pamsonkhanowu nkhani zina zidzakambidwa ndi mlendo woimira nthambi. Mutu wa msonkhanowu ndi wakuti “Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita.”

“Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita”

Pulogalamu ya nkhani zimene zidzakambidwa m’mawa komanso masana pa msonkhano wadera wokhala ndi woimira nthambi.

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mafunso awa adzayankhidwa pamene nkhani zikukambidwa.