Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2019-2020​—Wokhala ndi Woimira Nthambi

Onani pulogalamu ya msonkhano waderawu yosonyeza nkhani zimene woimira nthambi adzakambe. Mutu wa msonkhanowu ndi wakuti, “Muzikonda Yehova Ndi Mtima Wanu Wonse”

Muzikonda Yehova Ndi Mtima Wanu Wonse

Msonkhanowu utithandiza kuti tizikonda kwambiri Yehova komanso kuti tizisonyeza chikondi chopanda dyera.

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mafunso amenewa adzayankhidwa pa msonkhanowu.