Pulogalamu ya 2018-2019 ya Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova Wokhala ndi Woyang’anira Dera

Gwiritsani ntchito pulogalamuyi kuti mutsatire msonkhano wadera. Mutu wa msonkhanowu ndi wakuti ‘Khalani Olimba Mtima.’

Khalani Olimba Mtima

N’chifukwa chiyani zingativute kukhala olimba mtima, nanga n’chiyani chingatithandize kukhala ndi khalidwe limeneli?

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mafunsowa adzayankhidwa pa msonkhanowu.