Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2019 la Mboni za Yehova Padziko Lonse.

Onani lipoti losonyeza mmene ntchito yolalikira ya Mboni za Yehova yayendera kuyambira September 2018 mpaka August 2019.

Ziwerengero Zonse za 2019

Lipotili likusonyeza ntchito imene a Mboni za Yehova anagwira komanso ndalama zomwe anagwiritsa ntchito pogwira ntchito yolalikira padziko lonse.

Lipoti la Mayiko Komanso Madera la 2019

Lipotili likunena za chiwerengero cha a Mboni, kuchuluka kwa anthu amene anabatizidwa, opezeka pa Chikumbutso ndi zina.

Onaninso

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.