Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2018 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yolalikira kuyambira mu September 2017 mpaka August 2018.

Ziwerengero Zonse za 2018

Lipotili likusonyeza zinthu zimene a Mboni za Yehova achita pogwira ntchito yawo yolalikira padziko lonse komanso zinthu zimene agwiritsa ntchito.

Lipoti la 2018 la Mayiko Komanso Madera

Lipotili likuphatikizapo chiwerengero cha Mboni za Yehova, obatizidwa, opezeka pa Chikumbutso komanso zinthu zina.

Onaninso

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.