Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?

Kodi mayankhowo tingawapeze . . .

  • kwa asayansi?

  • kwa anthu anzeru?

  • m’Baibulo?

WOLEMBA BAIBULO WINA ANAPEMPHA MULUNGU KUTI,

“Ndithandizeni kukhala wozindikira . . . Mawu anu onse ndi choonadi.”​—Salimo 119:144, 160, Baibulo la Dziko Latsopano.

Baibulo likuyankha mafunso a anthu ambiri.

Kodi mungakonde kukhala ena mwa anthu amenewo?

Webusaiti ya jw.org ingakuthandizeni kuyankha mafunso anu.

WERENGANI zimene zili pa intaneti

ONERANI mavidiyo a nkhani za m’Baibulo

PANGANI DAWUNILODI mabuku

PA MAFUNSO OMWE ALI M’MUNSIWA, KODI NDI FUNSO LITI LOMWE MUMAFUNA MUTADZIWA YANKHO LAKE?

Pezani mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso amenewa pa webusaiti ya jw.org.

(Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)