Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

M’nthawi yovutayi, mabanja ambiri akusokonezeka. Koma kodi n’zotheka kukhala ndi banja losangalala? N’zoona kuti si zapafupi komabe pali zinthu zimene zingakuthandizeni. Ngakhale kuti kabukuka sikafotokoza zonse zimene banja lanu liyenera kuchita, kali ndi malangizo ndiponso mfundo zothandiza zochokera m’Baibulo. Kutsatira malangizo ndi mfundo zimenezi kungathandize kuti mukhale ndi banja losangalala.