Mfundo Zanga—Mtima Wanu
Chigawo 7
Mfundo Zanga—Mtima Wanu
Kodi ndi khalidwe liti limene limakuvutitsani kwambiri? Nanga lakhudza bwanji mmene mumachitira zinthu?
․․․․․
Kodi mungagwiritsire ntchito bwanji mfundo zimene mwapeza mu chigawo chino kuti muthane ndi khalidweli?
․․․․․