Mfundo Zanga—Kusirira Mnyamata Kapena Mtsikana
Chigawo 1
Mfundo Zanga—Kusirira Mnyamata Kapena Mtsikana
Ngati mukufuna kukwatira kapena kukwatiwa, lembani makhalidwe awiri ofunika kwambiri amene mukufuna kuti munthu ameneyo akhale nawo, ndipo fotokozani chifukwa chake. Ngati panopa simukufuna kulowa m’banja, lembani mfundo ziwiri zosonyeza ubwino wokhala wosakwatira kapena kukwatiwa.
․․․․․