Mfundo Zanga—Kusintha kwa Thupi
Chigawo 2
Mfundo Zanga—Kusintha kwa Thupi
Tchulani chinthu chimodzi chokhudza inuyo chimene chimakuipirani ndipo fotokozani chifukwa chake.
․․․․․
Tchulani chinthu chimodzi chokhudza inuyo chimene mumasangalala nacho kwambiri ndipo fotokozani chifukwa chake.
․․․․․