Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-F

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki wa Yesu Wakumapeto Kum’mawa kwa Yorodano

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki wa Yesu Wakumapeto Kum’mawa kwa Yorodano

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, pambuyo pa Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu

Betaniya wa kutsidya kwa Yorodano

Apita kumene Yohane ankabatizira; ambiri akhulupirira Yesu

     

10:40-42

Pereya

Aphunzitsa m’mizinda ndi m’midzi, alowera ku Yerusalemu

   

13:22

 

Awalimbikitsa kulowa pakhomo lopapatiza; adandaulira Yerusalemu

   

13:23-35

 

Mwina ku Pereya

Aphunzitsa kudzichepetsa; mafanizo: malo olemekezeka kwambiri ndi alendo omwe analephera kubwera ku phwando

   

14:1-24

 

Kuwerengera mtengo wa kukhala wophunzira

   

14:25-35

 

Mafanizo: nkhosa yotayika, ndalama yotaika, mwana wolowerera

   

15:1-32

 

Mafanizo: Mtumiki woyang’anira nyumba wosalungama, munthu wolemera ndi Lazaro

   

16:1-31

 

Aphunzitsa zokhudza kukhumudwitsana, kukhululukirana, ndi chikhulupiriro

   

17:1-10

 

Betaniya

Lazaro amwalira ndi kuukitsidwa

     

11:1-46

Yerusalemu; Efuraimu

Chiwembu chofuna kupha Yesu; achokako

     

11:47-54

Samariya; Galileya

Achiritsa akhate 10; aphunzitsa za Ufumu wa Mulungu

   

17:11-37

 

Samariya kapena Galileya

Mafanizo: mkazi wamasiye wolimbikira kupempha, Mfarisi ndi wokhometsa msonkho

   

18:1-14

 

Pereya

Aphunzitsa za ukwati ndi zokhudza kuthetsa ukwati

19:1-12

10:1-12

   

Adalitsa ana aang’ono

19:13-15

10:13-16

18:15-17

 

Funso la munthu wolemera; fanizo la antchito a m’munda wa mpesa ndi malipiro ofanana

19:16–20:16

10:17-31

18:18-30

 

Mwina ku Pereya

Kachitatu Yesu aneneratu za imfa yake

20:17-19

10:32-34

18:31-34

 

Kupemphera malo Yakobo ndi Yohane mu Ufumu

20:20-28

10:35-45

   

Yeriko

Podutsa achiritsa amuna awiri osaona; achezera Zakeyu; fanizo la ndalama 10 za mina

20:29-34

10:46-52

18:35–19:28