Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-E

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 3) ndi ku Yudeya

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 3) ndi ku Yudeya

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, pambuyo pa Pasika

Nyanja ya Galileya; Betsaida

Akukwera ngalawa n’kupita ku Betsaida, achenjeza za chofufumitsa cha Afarisi; achiritsa wosaona

16:5-12

8:13-26

   

Kaisareya wa Filipi

Makiyi a Ufumu; aneneratu za imfa yake ndi kuukitsidwa

16:13-28

8:27–9:1

9:18-27

 

Mwina pa phiri la Herimoni

Akusandulika; Mawu a Yehova akumveka

17:1-13

9:2-13

9:28-36

 

Kaisareya wa Filipi

Achiritsa mnyamata wogwidwa ndi ziwanda

17:14-20

9:14-29

9:37-43

 

Galileya

Aneneratunso za imfa yake

17:22, 23

9:30-32

9:43-45

 

Kaperenao

Ndalama yokakhomera msonkho iperekedwa mozizwitsa

17:24-27

     

Wamkulu kwambiri mu Ufumu; anena fanizo la nkhosa yosochera ndi la kapolo wosakhululuka

18:1-35

9:33-50

9:46-50

 

Galileya, Samariya

Pa ulendo wopita ku Yerusalemu, auza ophunzira kuika patsogolo za Ufumu

8:19-22

 

9:51-62

7:2-10

Utumiki wa Yesu Wakumapeto ku Yudeya

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, Chikondwerero cha Misasa

Yerusalemu

Aphunzitsa anthu pa Chikondwerero cha Misasa; asilikali atumidwa kuti amange Yesu

     

7:11-52

Anena kuti “Ine ndine kuwala kwa dziko”; achiritsa munthu wobadwa osaona

     

8:12–9:41

Mwina ku Yudeya

Atumwi 70 atumizidwa kukalalikira; abwerako akusangalala

   

10:1-24

 

Yudeya; Betaniya

Afotokoza za Msamariya wachifundo; apita kunyumba kwa Mariya ndi Marita

   

10:25-42

 

Mwina ku Yudeya

Aphunzitsanso pemphero lachitsanzo; anena fanizo lokhudza kulimbikira kupemphera

   

11:1-13

 

Achotsa ziwanda pogwiritsa ntchito chala cha Mulungu; akananso kusonyeza Alembi ndi Afarisi chizindikiro

   

11:14-36

 

Adya ndi Mfarisi; adzudzula chinyengo cha Afarisi

   

11:37-54

 

Fanizo la wachuma wopanda nzeru ndi la Mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika

   

12:1-59

 

Achiritsa mkazi wolumala pa Sabata; fanizo la kanjere ka mpiru ndi la zofufumitsa

   

13:1-21

 

32, Chikondwerero cha Kupereka Kachisi kwa Mulungu

Yerusalemu

Fanizo la M’busa wabwino; Ayuda ayesa kumuponya miyala; anyamuka n’kupita ku Betaniya wa kutsidya la Yorodano

     

10:1-39