Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-C

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 1)

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 1)

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

30

Galileya

Choyamba alengeza kuti “Ufumu wakumwamba wayandikira”

4:17

1:14, 15

4:14, 15

4:44, 45

Kana; Nazareti; Kaperenao

Achiritsa mnyamata; awerenga mpukutu wa Yesaya; akanidwa; apita ku Kaperenao

4:13-16

 

4:16-31

4:46-54

Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao

Aitana ophunzira anayi: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane

4:18-22

1:16-20

5:1-11

 

Kaperenao

Achiritsa apongozi a Simoni ndi ena

8:14-17

1:21-34

4:31-41

 

Galileya

Ulendo woyamba wozungulira mu Galileya ali ndi ophunzira anayi

4:23-25

1:35-39

4:42, 43

 

Wakhate achiritsidwa; anthu miyandamiyanda akhamukira kwa Yesu

8:1-4

1:40-45

5:12-16

 

Kaperenao

Achiritsa wakufa ziwalo

9:1-8

2:1-12

5:17-26

 

Kuitanidwa kwa Mateyu; achita phwando ndi okhometsa msonkho; afunsidwa funso lokhudza kusala kudya

9:9-17

2:13-22

5:27-39

 

Yudeya

Alalikira m’masunagoge

   

4:44

 

31, Pasika

Yerusalemu

Achiritsa mwamuna wina ku Betesida; Ayuda ayamba kufuna kumupha

     

5:1-47

Kubwerera kuchokera ku Yerusalemu (?)

Ophunzira abudula ngala za tirigu pa Sabata; Yesu ndi “Mbuye wa Sabata”

12:1-8

2:23-28

6:1-5

 

Galileya; Nyanja ya Galileya

Achiritsa dzanja pa Sabata; khamu la anthu liyamba kumutsatira; achiritsa anthu enanso ambiri

12:9-21

3:1-12

6:6-11

 

Phiri la pafupi ndi Kaperenao

Anthu 12 asankhidwa

 

3:13-19

6:12-16

 

Pafupi ndi Kaperenao

Ulaliki wa paphiri

5:1–7:29

 

6:17-49

 

Kaperenao

Achiritsa wantchito wa kapitawo

8:5-13

 

7:1-10

 

Naini

Aukitsa mwana wa mkazi wamasiye

   

7:11-17

 

Tiberiyo; Galileya (Naini kapena pafupi)

Yohane ali m’ndende atumiza ophunzira ake kwa Yesu; Yesu atamanda Yohane

11:2-30

 

7:18-35

 

Galileya (Naini kapena pafupi)

Mzimayi wochimwa athira mafuta pamapazi ake; fanizo la angongole

   

7:36-50

 

Galileya

Ulendo wachiwiri wolalikira m’Galileya ndi atumwi 12

   

8:1-3

 

Waziwanda achiritsidwa; tchimo losakhululukidwa

12:22-37

3:19-30

   

Alembi ndi Afarisi afuna kuona chizindikiro

12:38-45

     

Mayi ake a Yesu ndi mchimwene wake abwera; anena kuti achibale ake ndi ophunzira ake

12:46-50

3:31-35

8:19-21