Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-D

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 2)

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 2)

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

31 kapena 32

Kaperenao

Yesu afotokoza mafanizo a Ufumu

13:1-53

4:1-34

8:4-18

 

Nyanja ya Galileya

Aletsa mphepo yamkuntho ali m’ngalawa

8:18, 23-27

4:35-41

8:22-25

 

Dera la Gadara

Atumiza ziwanda kuti zikalowe mu nkhumba

8:28-34

5:1-20

8:26-39

 

Mwina ku Kaperenao

Achiritsa mayi wina wa nthenda yotaya magazi; Aukitsa mwana wamkazi wa Yairo

9:18-26

5:21-43

8:40-56

 

Kaperenao (?)

Achiritsa wosaona ndi wosalankhula

9:27-34

     

Nazareti

Akanidwanso mu mzinda wakwawo

13:54-58

6:1-5

   

Galileya

Ulendo wachitatu woyendera Galileya; madera ambiri ayenderedwa atatumiza atumwi

9:35–11:1

6:6-13

9:1-6

 

Tiberiyo

Herode adula mutu wa Yohane M’batizi; Herode achita mantha atamva za Yesu

14:1-12

6:14-29

9:7-9

 

32, Chikondwerero cha Pasika chitayandikira (Yoh. 6:4)

Kaperenao (?); Kumpoto chakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya

Atumwi abwerako pa ulendo wokalalikira; Yesu adyetsa amuna 5,000

14:13-21

6:30-44

9:10-17

6:1-13

Kumpoto chakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya; Genesarete

Anthu ayesa kulonga ufumu Yesu; ayenda panyanja; achiritsa anthu

14:22-36

6:45-56

 

6:14-21

Kaperenao

Afotokoza za “chakudya chopatsa moyo”; ophunzira ambiri akhumudwa ndi kusiya kum’tsatira

     

6:22-71

32, Pambuyo pa Pasika

Mwina ku Kaperenao

Afotokoza za miyambo ya anthu

15:1-20

7:1-23

 

7:1

Foinike; Dekapole

Achiritsa mwana wamkazi wa mayi wa ku Foinike; adyetsa anthu 4,000

15:21-38

7:24–8:9

   

Magadani

Asaduki ndi Afarisi afuna chizindikiro

15:39–16:4

8:10-12