Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-H

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu M’Yerusalemu (Gawo 2)

Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu M’Yerusalemu (Gawo 2)

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

Nisani 14

Yerusalemu

Yesu aulula kuti Yudasi ndi yemwe adzamupereke ndipo amuuza kuti achoke

26:21-25

14:18-21

22:21-23

13:21-30

Ayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (1Akor. 11:23-25)

26:26-29

14:22-25

22:19, 20, 24-30

 

Aneneratu za kukanidwa ndi Petulo ndi kubalalika kwa atumwi

26:31-35

14:27-31

22:31-38

13:31-38

Alonjeza mthandizi; fanizo la mpesa weniweni; apereka lamulo la chikondi; pemphero lomaliza ndi atumwi ake

     

14:1–17:26

Getsemane

Yesu avutika maganizo; aperekedwa ndi kumangidwa

26:30, 36-56

14:26, 32-52

22:39-53

18:1-12

Yerusalemu

Azengedwa mlandu ndi Anasi; ndi Kayafa, Khoti Lalikulu la Ayuda; Petulo am’kana

26:57–27:1

14:53–15:1

22:54-71

18:13-27

Yudasi wom’perekayo adzimangirira (Mac. 1:18, 19)

27:3-10

     

Aonekera kwa Pilato, kenako kwa Herode, ndi kubwereranso kwa Pilato

27:2, 11-14

15:1-5

23:1-12

18:28-38

Pilato ayesetsa kuti am’masule koma Ayuda akufuna awamasulire Baraba; aperekedwa kukapachikidwa pamtengo wozunzikirapo

27:15-30

15:6-19

23:13-25

18:39–19:16

(cha m’ma 3:00 madzulo, Lachisanu)

Gologota

Imfa ya Yesu pamtengo wozunzikirapo

27:31-56

15:20-41

23:26-49

19:16-30

Yerusalemu

Mtembo wa Yesu auchotsa pamtengo wozunzikirapo ndi kukauika m’manda

27:57-61

15:42-47

23:50-56

19:31-42

Nisani 15

Yerusalemu

Ansembe ndi Afarisi aika alonda pa manda ndi kutsekapo

27:62-66

     

Nisani 16

Yerusalemu ndi madera apafupi; Emau

Kuuka kwa Yesu; aonekera ka 5 kwa ophunzira ake

28:1-15

16:1-8

24:1-49

20:1-25

Pambuyo pa Nisani 16

Yerusalemu; Galileya

Aonekeranso maulendo angapo kwa ophunzira ake (1Akor. 15:5-7; Mac. 1:3-8); aphunzitsa; ndi kulamula kuti agwire ntchito yophunzitsa anthu

28:16-20

   

20:26–21:25

Iyari 25

Phiri la Maolivi, pafupi ndi Betaniya

Yesu akwera kumwamba, tsiku la 40 pambuyo pa kuuka kwake (Mac. 1:9-12)

   

24:50-53