Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 3-B

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

Mafumu a mu Ufumu Wakum’mwera (Kupitiriza)

777 B.C.E.

Yotamu: zaka 16

762

Ahazi: zaka 16

746

Hezekiya: zaka 29

716

Manase: zaka 55

661

Amoni: zaka ziwiri

659

Yosiya: zaka 31

628

Yehoahazi: miyezi itatu

Yehoyakimu: zaka 11

618

Yehoyakini: miyezi itatu ndi masiku 10

617

Zedekiya: zaka 11

607

Magulu a nkhondo a ku Babulo awononga Yerusalemu ndi kachisi wake motsogoleredwa ndi Nebukadinezara. Zedekiya, mfumu yomaliza yochokera mu mzere wa Davide, ichotsedwa pampando

 Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto (Kupitiriza)

M’ma 803 B.C.E.

Zekariya: Analamulira kwa miyezi 6 yokha

Tinganene kuti Zekariya anayamba kulamulira, koma zinali zisanatsimikizirike kuti ufumuwo ndi wake mpaka cha m’ma 792

M’ma 791

Salumu: mwezi umodzi

M’ma 780

Menahemu: zaka 10

Pekahiya: zaka ziwiri

M’ma 778

Peka: zaka 20

M’ma 758

Hoshiya: zaka 9 kuchokera cha m’ma 748

M’ma 748

Zikuoneka kuti ufumu wa Hoshiya unakhazikika mwina chifukwa ankathandizidwa ndi mfumu ya Asuri, Tigilati-pilesere Wachitatu cha m’ma 748

740

Asuri analanda Samariya, n’kuyamba kulamulira Aisiraeli, ufumu wa mafuko 10 wa Isiraeli unatha

 • Mayina a Aneneri

 • Yesaya

 • Mika

 • Zefaniya

 • Yeremiya

 • Nahumu

 • Habakuku

 • Danieli

 • Ezekieli

 • Obadiya

 • Hoseya