Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 12

Kachisi Womangidwa ndi Solomo

Kachisi Womangidwa ndi Solomo
 1.  Mbali za Kachisi

 2. 1 Malo Oyera Koposa (1 Maf. 6:16, 20)

 3. 2 Malo Oyera (2 Mbiri 5:9)

 4. 3 Zipinda Zakudenga (1 Mbiri 28:11)

 5. 4 Zipinda Zam’mbali (1 Maf. 6:5, 6, 10)

 6. 5 Yakini (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

 7. 6 Boazi (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

 8. 7 Khonde (1 Maf. 6:3; 2 Mbiri 3:4) (Kutalika kwake sikukudziwika bwinobwino)

 9. 8 Guwa Lansembe Lamkuwa (2 Mbiri 4:1)

 10. 9 Nsanja Yamkuwa (2 Mbiri 6:13)

 11. 10 Bwalo la Mkati (1 Maf. 6:36)

 12. 11 Thanki Yamkuwa (1 Maf. 7:23)

 13. 12 Zotengera Zamawilo (1 Maf. 7:27)

 14. 13 Khomo la M’mbali (1 Maf. 6:8)

 15. 14 Zipinda Zodyeramo (1 Mbiri 28:12)