Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 13

Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Oloseredwa ndi Danieli

Maulamuliro Amphamvu Padziko Lonse Oloseredwa ndi Danieli

Babulo

Danieli 2:32, 36-38; 7:4

607 B.C.E. Mfumu Nebukadinezara awononga Yerusalemu

Mediya ndi Perisiya

Danieli 2:32, 39; 7:5

539 B.C.E. Agonjetsa Babulo

537 B.C.E. Koresi alamula kuti Ayuda abwerere ku Yerusalemu

Girisi

Danieli 2:32, 39; 7:6

331 B.C.E. Alekizanda Wamkulu agonjetsa Perisiya

Roma

Danieli 2:33, 40; 7:7

63 B.C.E. Ayamba kulamulira Isiraeli

70 C.E. Awononga Yerusalemu

Britain ndi America

Danieli 2:33, 41-43

1914-1918 C.E. Britain ndi America ayamba kulamulira dziko lonse mkati mwa Nkhondo Yoyamba ya Padziko Lonse