Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 4-B

Zochitika Zikuluzikulu m’Moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu

Zochitika Zikuluzikulu m’Moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu

NTHAWI

MALO

CHOCHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

29, chakumapeto kwa chaka

Mtsinje wa Yorodano, mwina chapafupi kapena ku Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano

Ubatizo ndi kudzozedwa kwa Yesu; Yehova akulengeza kuti Yesu ndi Mwana wake ndipo akumuvomereza

3:13-17

1:9-11

3:21-38

1:32-34

Chipululu cha Yudeya

Yesu ayesedwa ndi Mdyerekezi

4:1-11

1:12, 13

4:1-13

 

Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano

Yohane M’batizi akunena za Yesu monga Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzira oyamba akuyamba kutsatira Yesu

     

1:15, 29-51

Kana wa ku Galileya; Kaperenao

Chozizwitsa choyamba cha Yesu, kusandutsa madzi kukhala vinyo; apita ku Kaperenao

     

2:1-12

30, Pasika

Yerusalemu

Athamangitsa amalonda m’kachisi

     

2:13-25

Yesu akambirana ndi Nikodemo

     

3:1-21

Yudeya; Ainoni

Apita kumadera a kumidzi a ku Yudeya, ophunzira ake abatiza anthu; Ulaliki womalizira wa Yohane wokhudza Yesu

     

3:22-36

Tiberiyo; Yudeya

Yohane aponyedwa m’ndende; Yesu anyamuka kupita ku Galileya

4:12; 14:3-5

6:17-20

3:19, 20

4:1-3

Sukari, ku Samariya

Ulendo wa ku Galileya, aphunzitsa Asamariya

     

4:4-43

Chipululu cha Yudeya