Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 9

Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

Mbali za Chihema Chopatulika

 1. 1 Likasa (Eks. 25:10-22; 26:33)

 2. 2 Nsalu Yotchinga (Eks. 26:31-33)

 3. 3 Mzati Wopachikirapo Nsalu Yotchinga (Eks. 26:31, 32)

 4. 4 Malo Oyera (Eks. 26:33)

 5. 5 Malo Oyera Koposa (Eks. 26:33)

 6. 6 Nsalu Yotchinga Khomo la Chihema (Eks. 26:36)

 7. 7 Mzati Wopachikirapo Nsalu Yapakhomo (Eks. 26:37)

 8. 8 Zitsulo za Mkuwa Zokhazikirapo Mizati (Eks. 26:37)

 9. 9 Guwa la Nsembe Zofukiza Zonunkhira (Eks. 30:1-6)

 10. 10 Tebulo ya Mkate Wachionetsero (Eks. 25:23-30; 26:35)

 11. 11 Choikapo Nyale (Eks. 25:31-40; 26:35)

 12. 12 Nsalu Zopangira Hema (Eks. 26:1-6)

 13. 13 Nsalu Zopangira Hema za Ubweya wa Mbuzi (Eks. 26:7-13)

 14. 14 Zikopa za Nkhosa Zophimbira (Eks. 26:14)

 15. 15 Zikopa za Akatumbu Zophimbira (Eks. 26:14)

 16. 16 Mafelemu Oimika (Eks. 26:15-18, 29)

 17. 17 Zitsulo Zasiliva Zokhazikapo Mafelemu Oimika (Eks. 26:19-21)

 18. 18 Mpingiridzo (Eks. 26:26-29)

 19. 19 Zitsulo Zasiliva Zokhazikapo Mizati (Eks. 26:32)

 20.  20 Beseni Losambira Lamkuwa (Eks. 30:18-21)

 21. 21 Guwa la Nsembe Zopsereza (Eks. 27:1-8)

 22. 22 Bwalo (Eks. 27:17, 18)

 23. 23 Chipata cha Bwalo (Eks. 27:16)

 24. 24 Nsalu Zotchinga za Ulusi Wopota Bwino (Eks. 27:9-15)

Mkulu wa Ansembe

Zovala za mkulu wa nsembe wachiisiraeli zinafotokozedwa mwatsatanetsatane mu Ekisodo 28