Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 19

Kalendala Yachiheberi

Kalendala Yachiheberi

NISANI (ABIBU) March​—April

Pa 14 Pasika

Pa 15-21 Mkate Wopanda Chofufumitsa

Pa 16 Nsembe ya zipatso zoyamba kucha

Yorodano amasefukira chifukwa cha mvula, ndi kusungunuka kwa madzi oundana

Balere

IYARA (ZIVI) April​—May

Pa 14 Pasika Wochitika Nthawi Yake Itadutsa

Chilimwe chikuyamba, kawirikawiri kumwamba kumakhala kopanda mitambo

Tirigu

SIVANI May​—June

Pa 6 Chikondwerero cha Masabata (Pentekosite)

Kunja kumatentha, mpweya wabwino

Tirigu, nkhuyu zoyambirira

TAMUZI June​—July

 

Kutentha kumawonjezeka. Kumagwa mame ambiri

Mphesa zoyambirira

ABA July​—August

 

Kutentha kumafika pachimake

Zipatso za m’chilimwe

ELULI August​—September

 

Kutentha kumapitirizabe

Zipatso za Kanjedza, mphesa ndi nkhuyu

TISHIRI (ETANIMU) September​—October

Pa 1 Tsiku loliza lipenga

Pa 10 Mwambo Wophimba Machimo

Pa 15-21 Chikondwerero cha Misasa

Pa 22 Msonkhano wapadera

Chilimwe chikutha, mvula yoyambirira ikuyamba kugwa

Kulima

HESHIVANI (BULU) October​—November

 

Mvula yowaza

Maolivi

KISILEVI November​—December

Pa 25 Chikondwerero cha Kupereka Kachisi kwa Mulungu

Mvula imawonjezeka, madzi amaundana m’mapiri

Ziweto zimakhala m’khola m’nyengo yozizira

TEBETI December​—January

 

Kumazizira kwambiri, kumagwa mvula madzi amaundana m’mapiri

Zomera zikukula

SEBATI January​—February

 

Kuzizira kumacheperako, mvula imapitiriza kugwa

Amondi wachita maluwa

ADARA February​—March

Pa 14, 15 Purimu

Kumachitikachitika mabingu ndi mvula ya matalala

Fulakesi

VEADARA March

Pa zaka 19 zilizonse, zaka 7 zinkakhala ndi mwezi wina wowonjezera