Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 18-B

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu Zomwe Zagwiritsidwa Ntchito M’malemba Achiheberi

Gera (1⁄20 ya sekeli)

magalamu 0.57 / 0.01835 oz t

Magera 10 = Beka imodzi

Beka

Magalamu 5.7 / 0.1835 oz t

Mabeka awiri = Sekeli imodzi

Pimu

Magalamu 7.8 / 0.2508 oz t

Pimu imodzi = 2⁄3 ya sekeli

Kulemela kwa Sekeli

Sekeli

Magalamu 11.4 / 0.367 oz t

Masekeli 50 = Mina imodzi

Mina

Magalamu 570 / 18.35 oz t

Mamina 60 = Talente imodzi

Talente

Makilogalamu 34.2 / 1,101 oz t

Dariki (imodzi ya ku Perisiya, yagolide)

Magalamu 8.4 / 0.27 oz t

Ezara 8:27

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu Zomwe Zagwiritsidwa Ntchito M’malemba Achigiriki

Leputoni (Ya Ayuda, yamkuwa)

1⁄2 kwadiransi

Luka 21:2

Kwadiransi (Ya Aroma, yamkuwa)

Maleputa awiri

Mateyu 5:26

Asariyoni (Aroma ndi madera ozungulira, yamkuwa)

4 kwadiransi

Mateyu 10:29

Dinari (Dinari imodzi ya Aroma, ya siliva)

64 kwadiransi

Magalamu 3.85 / 0.124 oz t

Mateyu 20:10

= Malipiro a tsiku limodzi (Maola 12)

Dirakima (imodzi ya Agiriki, ya siliva)

Magalamu 3.4 / 0.109 oz t

Luka 15:8

= Malipiro a tsiku limodzi (Maola 12)

Dirakima (Dirakima imodzi ya Agiriki, ya siliva)

Madirakima awiri

Magalamu 6.8 / 0.218 oz t

Mateyu 17:24

= Malipiro a masiku awiri

Tetiradirakima ya ku Antiokeya

Tetiradirakima ya ku Turo (Sekeli ya siliva ya ku Turo)

Tetiradirakima (Ya Agiriki, ya siliva; imatchedwanso siteta ya siliva)

Madirakima 4

Magalamu 13.6 / 0.436 oz t

Mateyu 17:27

= Malipiro a masiku 4

Mina

Madirakima 100

Magalamu 340 / 10.9 oz t

Luka 19:13

= Pafupifupi malipiro a masiku 100

Talente

Mamina 60

Makilogalamu 20.4 / 654 oz t

Mateyu 18:24

Chivumbulutso 16:21

= Pafupifupi malipiro a zaka 19

Paundi (ya Aroma)

Magalamu 327 / 11.5 oz

Yohane 12:3

“Mafuta onunkhira okwana magalamu 327, nado weniweni”