Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 18

Miyezo ya Zinthu Ndiponso Malonda

Miyezo ya Zinthu Ndiponso Malonda
 • Miyezo ya Zinthu Zamadzi

 • Kori (mitsuko 10 / mahini 60)

  Malita 220 / magaloni 58.1

 • Mtsuko (mahini 6)

  Malita 22 / magaloni 5.81

 • Hini (malogi 12)

  Malita 3.67 / mapainti 7.75

 • Logi (1 ⁄ 12 hini)

  Malita 0.31 / mapainti 0.66

 • Miyezo ya Zinthu Zomwe si Zamadzi

 • Homeri (kori imodzi / maefa 10)

  Malita 220 / makwati 200

 • Efa (maseya 3 / ma omeri 10)

  Malita 22 / makwati 20

 • Seya (ma omeri 31 ⁄ 3)

  Malita 7.33 / makwati 6.66

 • Omeri (makabu 14 ⁄ 5)

  Malita 2.2 / makwati awiri

 • Kabu

  Malita 1.22 / makwati 1.11

 • Kwati

  Malita 1.08 / makwati 0.98

 •  Miyezo Yoyezera Mtunda

 • Bango lalitali (Mikono 6)

  Mamita 3.11 / Mafiti 10.2

 • Bango (Mikono 6)

  Mamita 2.67 / Mafiti 8.75

 • Fatomu

  Mamita 1.8 / Mafiti 6

 • Mkono umodzi (Zikhatho 7)

  Masentimita 51.8 / Mainchesi 20.4

 • Mkono (Masipani 2 / Zikhatho 6 )

  Masentimita 44.5 / Mainchesi 17.5

 • Mkono waufupi

  Masentimita 38 / Mainchesi 15

 • Bwalo lachiroma

  1 ⁄ 8 ya mailo yachiroma=Mamita 185 / Mafiti 606.95

 1. 1 Mphipi imodzi ya chala (1 ⁄ 4 ya chikhatho)

  Masentimita 1.85 / Mainchesi 0.73

 2. 2 Chikhatho (Mphipi ya zala 4)

  Masentimita 7.4 / Mainchesi 2.9

 3. 3 Sipani (Zikhatho 3)

  Masentimita 22.2 / Mainchesi 8.75