Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019

Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova wa 2019 wakuti “Chikondi Sichitha.”

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa 1 Atesalonika 4:9​—‘Mulungu amatiphunzitsa kukondana.’

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Aefeso 5:2​—“Yendanibe m’chikondi.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Yuda 21​—“Pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.”

Mawu kwa Osonkhana

Dziwani zoyenera kuchita pa msonkhano wachigawo.