Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 ZIMENE ZACHITIKA M’CHAKA CHAPITACHI

Kodi Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwanji ku Warwick?

Kodi Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwanji ku Warwick?

NTCHITO yomanga maofesi omwe adzakhale likulu lathu ku Warwick, ku New York ikuyenda bwino kwambiri. Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova akudalitsa ntchitoyi.

M’bale Anthony Morris, yemwe ali m’Bungwe Lolamulira, ananena kuti abale amene adzabwere kudzaona maofesiwa ntchitoyi ikadzatha adzawalandira ndi manja awiri.

Malo olowera ku likulu lathu latsopano ku Warwick, ku New York