Pitani ku nkhani yake

Yehova Anapitiriza Kusonyeza Chikondi Chokhulupirika

Muvidiyoyi, onani mmene Yosefe anasonyezera kuti ankakonda kwambiri Mulungu komanso anthu ena ngakhale kuti ankakumana ndi mavuto. Onaninso mmene Yehova anamusonyezera chikondi chokhulupirika pa nthawi yonse imene ankakumana ndi mayeserowo. Yachokera pa Genesis 37:1-36; 39:1–47:12.