Pitani ku nkhani yake

“Limba Mtima, Ugwire Ntchitoyi Mwamphamvu”

Munthu amene amakhulupirira kwambiri Yehova amakhalabe wolimba akakumana ndi mavuto. Onerani vidiyoyi yomwe ili ndi mbali ya kuwerenga Baibulo mwasewero, kuti mumve zimene Davide anachita posonyeza kuti anali ndi chikhulupiriro.

Nkhaniyi yachokera pa 1 Mbiri 28:1-20; 1 Samueli 16:1-23; 17:1-51