Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

October 2-8

DANIELI 7-9

October 2-8
 • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • ‘‘Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike’’: (10 min.)

  • Dan. 9:24​—Nsembe ya Mesiya inathandiza kuti machimo a anthu akhululukidwe (it-2 902 ¶2)

  • Dan. 9:25​—Mesiya anafika kumapeto kwa mlungu wa 69 wa milungu yoimira zaka (it-2 900 ¶7)

  • Dan. 9:26, 27a​—Mesiya anaphedwa pakatikati pa mlungu wa 70 wa milungu yoimira zaka (it-2 901 ¶2, 5)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Dan. 9:24​—Kodi kudzoza “Malo Opatulikitsa” kunachitika liti? (w01 5/15 27)

  • Dan. 9:27​—Kodi ndi pangano lotani limene anasungira anthu ambiri mpaka kumapeto kwa mlungu wa 70 wa milungu yoimira zaka, kapena kuti mu 36 C.E.? (w07 9/1 20 ¶4)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 7:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Limbikitsani ofalitsa kuti aziyesetsa kubwerera mwamsanga kwa anthu amene anasonyeza chidwi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU