Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 7-8

Nyamula Mtengo Wako Wozunzikirapo, ndi Kunditsatira Mosalekeza

Nyamula Mtengo Wako Wozunzikirapo, ndi Kunditsatira Mosalekeza

8:34

Yesu ananena kuti, ‘tizimutsatira mosalekeza.’ Kuti tikwanitse kuchita zimenezi timafunika tizipirira. Kodi tingachite bwanji zimenezi pa nkhani ya . . .

  • kupemphera?

  • kuphunzira Mawu a Mulungu?

  • kulalikira?

  • kusonkhana?

  • kuyankha pamisonkhano?