Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu

Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu

ONERANI VIDIYO YAKUTI YEHOVA SANGAIWALE CHIKONDI CHANU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi munthu akamakalamba amakumana ndi mavuto otani?

  • Kodi ndi makhalidwe abwino ati amene okalamba ambiri amakhala nawo?

  • Ngati ndinu wokalamba, kodi malemba a Levitiko 19:32 ndi Miyambo 16:31 angakulimbikitseni bwanji?

  • Kodi Yehova amawaona bwanji atumiki ake okalamba omwe sangathe kuchita zambiri pomutumikira?

  • Kodi Yehova amafuna kuti tizichita chiyani ngakhale titakalamba?

  • Kodi okalamba angalimbikitse bwanji achinyamata?

  • Kodi posachedwapa m’bale kapena mlongo wokalamba wakulimbikitsani bwanji?