Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

May 8-14

YEREMIYA 35-38

May 8-14
  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.3 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.3 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl phunziro 26

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 127

  • Kusamalira Malo Athu Olambirira: (15 min.) Nkhani ya mafunso ndi mayankho ndipo ikambidwe ndi mkulu. Pambuyo poonetsa vidiyo yakuti Kusamalira Malo Athu Olambirira komanso kukambirana mafunso, kambiranani mwachidule ndi m’bale amene ali m’komiti yoyang’anira Nyumba ya Ufumu. (Ngati palibe, funsani wogwirizanitsa ntchito za akulu. Ngati Nyumba ya Ufumuyo imagwiritsidwa ntchito ndi mpingo wanu wokha, funsani m’bale woyang’anira ntchito yosamalira Nyumba ya Ufumu.) Kodi ndi ntchito yosamalira Nyumba ya Ufumu yotani imene yachitika posachedwapa, ndipo pakonzedwa zotani kutsogoloku? Ngati pa mpingopo pali ena amene ali ndi luso, kapena amene akufuna kuphunzira lusolo kwa amene ali nalo kale, kodi ayenera kuchita chiyani? Kodi aliyense mumpingo angathandize bwanji kusamalira Nyumba ya Ufumu?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 23 ¶15-29 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 204

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero