Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 49-50

Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza

Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza

50:4-7

  • Aisiraeli omwe analapa anasangalala Yehova atawamasula ku ukapolo

  • Iwo anabwerezanso pangano lawo lomwe anachita ndi Yehova ndipo anabwerera ku Yerusalemu n’kukayambiranso kulambira Mulungu

50:29, 39

  • Ababulo omwe anali odzikuza, analangidwa chifukwa ankachitira nkhanza anthu a Yehova

  • Monga mmene ulosi unanenera, Babulo anakhala bwinja