Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

May 29–June 4

YEREMIYA 49-50

May 29–June 4
 • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza”: (10 min.)

  • Yer. 50:4-7—Aisiraeli odzichepetsa omwe analapa anamasulidwa ku ukapolo ndipo anabwerera ku Ziyoni

  • Yer. 50:29-32—Babulo anawonongedwa chifukwa chochita zinthu modzikuza (it-1 54)

  • Yer. 50:38, 39—M’Babulo simudzakhalanso anthu (jr 161 ¶15; w98 4/1 20 ¶20)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 49:1, 2—N’chifukwa chiyani Yehova anadzudzula a Amoni? (it-1-E 94 ¶6)

  • Yer. 49:17, 18—Kodi Edomu anafanana bwanji ndi Sodomu ndi Gomora, ndipo n’chifukwa chiyani? (jr 163 ¶18; ip-2 351 ¶6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 50:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-32—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-32—Kambiranani kachigawo kakuti “Ganizirani Mfundo Iyi.” Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w15 3/15 17-18—Mutu: N’chifukwa Chiyani Masiku Ano Mabuku Athu Safotokoza Kwambiri Kuti Zinthu Zosiyanasiyana Zotchulidwa m’Baibulo Zimaphiphiritsira Zinazake?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 64

 • Chotsa Mtanda wa Denga M’diso Lako: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Chotsa Mtanda wa Denga M’diso Lako. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi m’bale wina wasonyeza bwanji kuti anali wonyada komanso wokonda kuweruza ena? N’chiyani chamuthandiza kuti asinthe maganizo? Nanga kodi wapindula bwanji?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 1 ¶11-20

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero