Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 32-34

Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo

Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo
ONANI

32:9-14

  • Yeremiya anatsatira malamulo ofunika pogula munda.

33:10, 11

  • Yehova anasonyeza kuti ndi wabwino polonjeza anthu ake omwe anali ku ukapolo kuti akamvera malangizo ake, adzawakhululukira ndipo adzabwerera ku Isiraeli.

Kodi Yehova wasonyeza bwanji kuti ndi wabwino kwa inuyo?