Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 26-33

Tizidalira Yehova Kuti Tikhale Olimba Mtima

Tizidalira Yehova Kuti Tikhale Olimba Mtima

Davide analimba mtima chifukwa chokumbukira mmene Yehova anamupulumutsira

27:1-3

  • Yehova anapulumutsa Davide kwa mkango

  • Yehova anathandiza Davide kupha chimbalangondo kuti ateteze nkhosa

  • Yehova anathandiza Davide kupha Goliyati

Kodi n’chiyani chingatithandize kukhala olimba mtima ngati Davide?

27:4, 7, 11

  • Pemphero

  • Kulalikira

  • Kupezeka pamisonkhano

  • Kuphunzira Baibulo patokha komanso kulambira kwa pabanja

  • Kulimbikitsa ena

  • Kukumbukira mmene Yehova anatithandizira nthawi ina m’mbuyomu