Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

May 2-8

YOBU 38-42

May 2-8
 • Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Amasangalala Tikamapempherera Ena”: (10 min.)

  • Yobu 42:7, 8—Yehova ankayembekezera kuti Yobu apempherere Elifazi, Bilidadi ndi Zofari (w13 6/15 21 ndime 17; w98 5/1 30 ndime 3-6)

  • Yobu 42:10—Yobu atawapempherera, Yehova anamupatsanso moyo wathanzi ngati mmene analili poyamba (w98 5/1 31 ndime 3)

  • Yobu 42:10-17—Yehova anadalitsa kwambiri Yobu chifukwa chakuti anali ndi chikhulupiriro komanso anali wopirira (w94 11/15 20 ndime 19-20)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 38:4-7—Kodi “nyenyezi za m’mawa” ndi ndani, nanga tikudziwa zotani zokhudza iwowo? (bh 97 ndime 3)

  • Yobu 42:3-5—Kodi ifeyo tingatani kuti tiziona Mulungu ngati mmene Yobu anachitira? (w15 10/15 8 ndime 16-17)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yobu 41:1-26

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse payokha, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Kenako pokambirana mmene tingagwiritsire ntchito chipangizo chamakono, tchulani mwachidule mfundo za m’nkhani yakuti, “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW.” Kumbutsani ofalitsa kuti kumapeto kwa mwezi uliwonse asamaiwale kulemba lipoti la maulendo omwe anaonetsako munthu vidiyo mu utumiki. Limbikitsani ofalitsa kuti alembe ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU