Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 12-18

Mateyu 22-23

March 12-18

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzitsatira Malamulo Awiri Aakulu Kwambiri”: (10 min.)

    • Mat. 22:36-38​—Kodi mavesi amenewa akusonyeza kuti kumvera lamulo lalikulu kwambiri m’Chilamulo kumaphatikizapo chiyani? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “mtima,” “moyo,” “maganizo” pa Mat. 22:37, nwtsty)

    • Mat. 22:39​—Kodi lamulo lalikulu lachiwiri ndi liti? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “Lachiwiri,” “mnzako” pa Mat. 22:39, nwtsty)

    • Mat. 22:40​—Mfundo za m’Malemba Achiheberi zagona pa chikondi (Mfundo zimene ndikuphunzira za “Chilamulo . . . Zolemba za Aneneri,” “chagona” pa Mat. 22:40, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 22:21​—Kodi “zinthu za Kaisara” ndi ziti, nanga “za Mulungu” ndi ziti? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “zinthu za Kaisara kwa Kaisara,” “za Mulungu” pa Mat. 22:21, nwtsty)

    • Mat. 23:24​—Kodi mawu a Yesu amenewa akutanthauza chiyani? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “amene mumasefa zakumwa zanu kuti muchotsemo kanyerere koma mumameza ngamila” pa Mat. 23:24, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 22:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 199 ¶8-9​—Limbikitsani wophunzira Baibulo wanu kuti aitanire anzake ku mwambo wa Chikumbutso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU