Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 5-7

Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna

Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna

7:1-4, 8-10, 15

  • Yeremiya anaulula molimba mtima machimo ndiponso chinyengo cha Aisiraeli

  • Aisiraeli ankaganiza kuti kachisi ali ndi mphamvu inayake yapadera yoti ingawateteze

  • Yehova anawauza kuti nsembe zimene ankapereka mwamwambo sizingachotse machimo awo

Dzifunseni kuti: Kodi ndingatani kuti ndizilambira Yehova mogwirizana ndi zimene amafuna osati mwamwambo chabe?

Yeremiya waima pachipata cha nyumba ya Yehova