Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 13-19

YEREMIYA 5-7

March 13-19
 • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna”: (10 min.)

  • Yer. 6:13-15—Yeremiya anaulula machimo a Aisiraeli (w11 3/15 29 ¶4; w88 4/1 11-12 ¶7-8)

  • Yer 7:1-7—Yehova anayesetsa kuwathandiza kuti alape (w88 4/1 12 ¶9-10; jr 70 ¶8)

  • Yer 7:8-15—Aisiraeli ankaganiza kuti Yehova sangachite chilichonse (jr 21 ¶12)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer 6:16—Kodi Yehova ankalangiza anthu ake kuti achite chiyani? (w05 11/1 23 ¶11)

  • Yer 6:22, 23—N’chifukwa chiyani Yeremiya ananena kuti “anthu akubwera kuchokera kudziko la kumpoto”? (w88 4/1 13 ¶15)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 5:26-31; 6:1-5

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.)T-36 Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-36 Kambiranani“mbali yakuti “Ganizirani Mfundo Iyi.” Muitanireni ku Chikumbutso.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 1—Muitanireni ku Chikumbutso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU