Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

June 20-26

MASALIMO 45-51

June 20-26
 • Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Sadzasiya Anthu Amtima Wosweka”: (10 min.)

  • Sal. 51:1-4—Davide anadzimvera chisoni kwambiri chifukwa chochimwira Yehova (w93 3/15 10-11 ndime 9-13)

  • Sal. 51:7-9—Davide ankafuna kuti Yehova amukhululukire kuti ayambirenso kukhala mosangalala (w93 3/15 12-13 ndime 18-20)

  • Sal. 51:10-17—Davide ankadziwa kuti Yehova amakhululukira munthu ngati walapa mochokera pansi pamtima (w15 6/15 14 ndime 6; w93 3/15 14-17 ndime 4-16)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 45:4—Kodi ndi mfundo yofunika kwambiri iti ya choonadi yomwe ikufunika kutetezedwa? (w14 2/15 5 ndime 11)

  • Sal. 48:12, 13—Kodi mavesiwa akutipatsa udindo wotani? (w15 7/15 9 ndime 13)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 49:10–50:6

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU