Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

July 30–August 5

Luka 14-16

July 30–August 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Fanizo la Mwana Wolowerera”: (10 min.)

  • Luka 15:11-16​—Mwana wolowerera anawononga cholowa chake pochita makhalidwe oipa (“Munthu wina anali ndi ana aamuna awiri” “Wamng’ono” “anasakaza” “m’makhalidwe oipa” “kuti azikaweta nkhumba” “chakudya cha nkhumba” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 15:11-16, nwtsty)

  • Luka 15:17-24​—Iye anadzimvera chisoni ndipo bambo ake anamuchitira chifundo n’kumulandiranso (“ndachimwira inu” “aganyu” “anamupsompsona mwachikondi” “kutchedwa mwana wanu” “mkanjo . . . mphete . . . nsapato” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 15:17-24, nwtsty)

  • Luka 15:25-32​—Bambo anathandiza mwana wake wamkulu kuti ayambe kuona zinthu moyenera

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Luka 14:26​—Kodi mawu akuti ‘kudana’ pavesili akutanthauza chiyani? (“osadana” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 14:26, nwtsty)

  • Luka 16:10-13​—Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena za “chuma chosalungama”? (w17.07 8-9 ¶7-8)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 14:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 32 ¶14-15

MOYO WATHU WACHIKHRISTU