Nowa ndi banja lake akukonzekera kulowa m’chingalawa

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU January 2020

Zimene Tinganene

Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza dzina la Mulungu, khalidwe lake lalikulu komanso zimene munthu angachite kuti akhale naye pa ubwenzi.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi

Kodi Yehova anapanga chiyani patsiku lililonse lolenga zinthu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira?

Kodi tiyenera kuchita zinthu ziwiri ziti tisanayambe kufotokozera munthu wina chifukwa chake timakhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mavuto Omwe Anabwera Chifukwa cha Bodza Loyamba

Satana, yemwe ndi tate wake wa bodza akupitirizabe kusocheretsa anthu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Tingayambe Bwanji Kukambirana ndi Anthu Pogwiritsa Ntchito Timapepala?

Kodi mungagwiritse ntchito bwanji kapepala poyamba kukambirana ndi munthu mu utumiki?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Anachitadi Momwemo”

Kodi tingaphunzire chiyani kwa Nowa pa nkhani ya kumvera, kukhulupirika komanso kugwira ntchito mwakhama?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Dziko Lonse Lapansi Linali ndi Chilankhulo Chimodzi”

Kodi n’chiyani chinachititsa kuti dziko lapansi ligawanike chifukwa cha chinenero? Kodi Mulungu akugwirizanitsa bwanji atumiki ake ochokera m’mitundu komanso zinenero zosiyanasiyana?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzigwira Ntchito Yanu Mwaluso

Zinthu zomwe timagwiritsa ntchito pophunzitsa zinakonzedwa kuti zizitithandiza mu utumiki. Kodi mumadziwa mmene mungazigwiritsire ntchito?