Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

January 30–February 5

YESAYA 43-46

January 30–February 5
 • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona”: (10 min.)

  • Yes. 44:26-28—Yehova analosera kuti Yerusalemu ndiponso kachisi adzamangidwanso komanso kuti Koresi ndi amene adzagonjetse Babulo (ip-2 71-72 ¶22-23)

  • Yes. 45:1, 2—Yehova ananeneratu mmene Babulo adzagonjetsedwere (ip-2 77-78 ¶4-6)

  • Yes. 45:3-6—Yehova anafotokoza chifukwa chake anagwiritsa ntchito Koresi kuti agonjetse Babulo (ip-2 79-80 ¶8-10)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 43:10-12—Kodi Aisiraeli anayenera kuchita chiyani kuti akhale mboni za Yehova? (w14 11/15 21-22 ¶14-16)

  • Yes. 43:25—Kodi chifukwa chachikulu chimene Yehova amafafanizira zolakwa zathu n’chiyani? (ip-2 60 ¶24)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 46:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) kt—Kulalikira mnzanu wakusukulu kapena wakuntchito.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) kt—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU