Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

January 23-29

YESAYA 38-42

January 23-29
 • Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Amapereka Mphamvu kwa Munthu Wotopa”: (10 min.)

  • Yes. 40:25, 26—Yehova ndi amene amapereka mphamvu (ip-1 409-410 ¶23-25)

  • Yes. 40:27, 28—Yehova amadziwa mavuto amene tikulimbana nawo komanso zinthu zopanda chilungamo zimene zikutichitikira (ip-1 413 ¶27)

  • Yes. 40:29-31—Yehova amapereka mphamvu kwa anthu omudalira (ip-1 413-415 ¶29-31)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 38:17—Kodi Yehova amaponyera bwanji machimo athu kumbuyo kwake? (w03 7/1 18 ¶17)

  • Yes. 42:3—Kodi Yesu anakwaniritsa bwanji ulosiwu? (w15 2/15 8 ¶13)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 40:6-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) kt—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) kt—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 38-39 ¶6-7—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 68

 • Tisamaiwale Kupempherera Akhristu Amene Akuzunzidwa”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti Kuzengedwanso kwa Mlandu wa a Mboni za Yehova ku Taganrog—Kodi Nkhanza Zimenezi Zidzatha?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 16 ¶1-15.

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero